97.The Power, Fate

  1. Ndithudi tinavumbulutsa ilo mu usiku wamphamvu
  2. Kodi ndi chiyani chimene chingakuuzeni kuti mudziwe kuti usiku wamphamvu ndi otani
  3. Usiku wamphamvu ndi wabwino kuposa miyezi chikwi chimodzi
  4. Mu usiku umenewu Angelo ndi Mzimu, ndi chilolezo cha Mulungu, amachoka kumwamba ndi kutsika pansi ndi malamulo ake onse
  5. Mtendere mpaka m’mbandakucha