94.The Consolation

  1. Kodi Ife sitidatsegule chifuwa chako
  2. Ndi kukuchotsa katundu wako wolemera
  3. Amene amalemetsa msana wako
  4. Ndipo tidakweza mbiri yako yabwino
  5. Ndithudi m’mavuto muli chithandizo
  6. Ndithudi m’mavuto muli chithandizo
  7. Ndipo pamene wamaliza, pembedza Mulungu
  8. Ndipo dzipereke kwathunthu kwa Ambuye wako