112.Sincerity

  1. Nena: Iye ndi Mulungu, mmodzi
  2. Mulungu, Mwini Mphamvu zonse
  3. Iye sabereka ndipo Iye sadaberekedwe
  4. Ndipo palibe wina wofanana naye